26/03/2026
zabwino zimayamba ndinu akasitomalaπ€ see quality iwe ππ0882259956
Gulani katundu aliyense wa furniture wapamwamba, wa kumtima kwanu kuchokela ku infix interiors Malawi.
call or wap: 0 882 25 99 56
Discover more and get a free quotation here: https://infix-interiors-mw.wuaze.com
26/03/2026
zabwino zimayamba ndinu akasitomalaπ€ see quality iwe ππ0882259956
14/02/2026
sizogula sokosi ayi apangisileni kitchen units okondedwa anuwo π
happy valentines day to our beautiful customers
01/11/2025
yambani mwezi wanu ndi furniture yamakono from Infix Interiors Mw
15/10/2025
Tikutitu kupeleka Ka wili pa mtengo wa wabwino
Big shout out to my newest top fans! Cosmas Hastings
23/07/2025
PREMIUM TV STANDS.
TV Stand isamachititse manyazi.
Smartness idziyambila mnyumba
Tapezani ka tv Stand ku Infix Interiors Mw pa ntengo wabhoo.
Tonse ndi A Malawi Osaopa
Olo kungofusa kokha fusani we are here for you gyz β¨
DEAL?
Message Us Now. π€
21/07/2025
NTCHITO INALI BWANJI?
Ku Office kumaoneka bwaa?
Zonse Zinali mchimake?
Zaguleni office furniture ku Infix Interiors Mw Ntchito imakoma mu office mukamakongola.
Office isamachititse manyaziii.
DEAL?
π€ MESSAGE US NOW.
21/07/2025
LERO MONDAY
tsiku lobwelera kuntchito after weekend.
Kod mu office mwanu muli kiliye???
Ma files Ali posamalika?
Computer mwakhazika pa desk labwino?
Nanga inuyo muli ndi mpando osatopesa mukakhala?
Office idziwala Inu aaah π€ .
Tiyankhuleni Ife aInfix Interiors Mw mupeze katundu wabwino ogwilizana ndi office yanuyo.
DEAL?
π€
Send Us Message Now.
20/07/2025
A Kasi anasangalala office itabeba ndi ma office desk opangidwa ndi Infix Interiors Mw
Pezan furniture iliyonse ya mu office kwa Ife.
Katundu olimba opangidwa ndi materials abwino, katundu okongola koma kamtengo pang'ono π².
Ma office desk, mipando, file racks, reception desk/table etc. Tiyankhulani Ife simudzakhumudwa.
20/07/2025
NDANI SAAFUNA KUGONA PABWINO? π€
King and Queen Size Beds.
Headboard massive
Ma drawers mbambande
Lotakasuka.
Tiyankhulani ku inbox ku mupeze lanu bed Design iliyonse timapanga π€
Infix Interiors Mw siisewela pa ntchitoooo!
| Monday | 09:00 - 17:00 |
| Tuesday | 09:00 - 17:00 |
| Wednesday | 09:00 - 17:00 |
| Thursday | 09:00 - 17:00 |
| Friday | 09:00 - 17:00 |
| Saturday | 09:00 - 17:00 |