Zayn Cement Blocks and Mobile Service

Zayn Cement Blocks and Mobile Service

Share

This is a blick laying company that specializes in molding cement blocks. We are situated in Mzuzu, Malawi and we travel to places upon booking.

Prices are charged upon a dialogue with the customer. Contact us on 0996469915 for more info.

24/09/2024

Mukafuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ifeyo a Zayn Cement Blocks ndipo simudzakhumudwa. Mtengo ndi okambilana. Muchedweranji ife tilipo?

23/08/2024

Zayn mobile service ikuthokoza kwa onse amene akupeza ma blocks ku kampani imeneyi motelo asisilathu mitengo yama services yawoyose, bwelani popeza zabwino sizichedwa kutha axanu akutenga

Photos from Zayn Cement Blocks and Mobile Service's post 05/08/2024

Ngati mukufuna ma cement blocks olimba, tipedzeni ndipo simudzakhumudwa.

Timakafika kulikonse komwe mukufuna kuti tikagwire ntchito ndipo mtengo ndi okambilana. Tikupedzeka mu mzinda wa Mzuzu koma mukafuna kumva zambiri, imbani phone pa 0996469915.

Want your business to be the top-listed Furniture Store in Mzuzu?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address

Mzuzu