The Trendè House

The Trendè House

Share

For all your furniture solutions. And also bring life to your old pieces at very affordable price

16/07/2026

Akasi kwacha bwanji kumeneko. Ife ndiye tayala malonda kwatichera.
Lero musankhapo chani?
Pali ma Tv stand, ma sofa, ma bed, ma console table, ma coffee table zonse mmene mungasankhire.😊
Choose a piece for your living spaces.
Choice assorted furniture.
Contact number 0994702191

13/07/2026

Good Morning Monday.
Kwacha Akasi. Tayala malonda zasankheni basi.
Contact number 0994702191

09/07/2026

Akasi sofa imeneyi bwanji pa seating room panupo bwanji?
Kukhalira zofewa bwino osati paziuma ngati mwakhalira crate ya chibuku🤣🤣
Umenewu uli pa K3,950,000
Number ndi 0994702191. Tili ku Nyambadwe Blantyre.

06/07/2026

Kodi ku project zili pati Akasi?
Menemotu mufunika ma kitchen unit, ndima bedroom wardrobes.
Tiitaneni tizayeze tikupase quotation tikagule materials tiyambepo.
Mitengo imatengera space yapamalopo.
Number ndi 0994702191

03/07/2026

Akasi katundu ndiye sankhani chilichonse chilipo.
Mundiuza ndi inu kuti chikhale chiti.
Dressing tables, console tables, coffee tables, sofas.
Tili pa 0994702191.
Mitengo ku comment section.

03/07/2026

Mpando wanu ujatu uwu akasi.
Specially made for your living room.
Good fabric and good finishing
3-2-1 going for K4,000,000
0994702191

30/06/2026

Sofa set ndi dinning table delivered in nkhotakota through use of courier.
All set in white sheep boucle.
Akuti ana ali nawo koma anawo amasamba sakadesa🤣
Contact number 0994702191
Sofa set K5,000,000
Dinning table K2,150,000

27/06/2026

Akasi ma sofa mukugula kuti?
Osasocheratu zabwino zilipo.
Ma sofa abwino kukhalira zaka zaka mpaka kutopa nawo😅
Umenewu ndi K4,500,000
Number ndi 0994702191.

24/06/2026

Akasi basi ntchito sitikusintha, ntchito ndiyomweyi.
Nanga ndingalime? 🤣🤣
Console Table imeneyi akasi K450,000
Nyambadwe Blantyre 0994702191

22/06/2026

Good morning Monday,
Kwacha bwanji kumeneko Akasi.
Sankhanipo kamodzi kokha mukonze nyumba Akasi.
Ka Chest of drawer mwakaona koma?

Want your business to be the top-listed Furniture Store in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Nyambadwe
Blantyre