Starise Furniture & Home Decor

Starise Furniture & Home Decor

Share

We are in Lilongwe near cashbuild Orange building opposite Malawi Housing shop #7 where there is Malawi housing

Photos from Max & Sherry Dine and Lounge's post 13/05/2026

Thank you partner Max & Sherry Dine and Lounge ndi ma partner onse one mukuonetsa love ku STARISE

09/05/2026

Congratulations kwa onse omwe apata tray yokongolayi kutengera engagement yawo pa page pathu week imeneyi(weekly engagement list yomwe facebook yatipatsa) Madalitso Majiya
Chisomo Nyirenda Nyakaunga Misozi Chirwa and Beatrice Zingwangwa I will add the 6th one for being the first one to tag the products she got from our shop Maggie Msiska mwakwana pitilizani kuikonda STARISE nonse.

Kuti mutenge tray yanu imbani

0999629159 or visit our shops in area 4 near Cashbuild pomwe pali sunset funeral services shop #7 or kapena Fikani ku work shop yathu ku gulliver nsewu wa Babtist mukamapita ku Padre pio pa hump yachiwiri kumanja

09/05/2026

Mwadzuka bwanji ma partner. Lero anthu 5 apite ndi ma tray 5 okongolawa tingatengere chani popereka kwa oikonda STARISE.

08/05/2026

Mpando Uwu ainiake anvekere ndimafuna ndingoutaya ife Tati komatu tikhoza kuukonza muzaudabwa. Sanakhulupilire kuti ungaoneke chonchi nanuso Tabweretsani wanu usandulike. Mitengo imatengera design ndi nsalu yomwe mukufuna. Mwakoma nonse

Phone πŸ“ž 0999629159

08/05/2026

Partner yemwe anabwera ku shop kwathu kugula set ya Mpando lero this morning apart from discount yomwe takupatsani mubwere muzatenge ma cushion covers 5 aulere mpando ukawale.

MaxSherians you are the best partnership ikuyenda bwino Kwambiri 😍

Photos from Starise Furniture & Home Decor's post 08/05/2026

Taonani taonani mipando ina mwa mipando yonse tinasintha πŸ₯°πŸ₯°

Photos from Starise Furniture & Home Decor's post 08/05/2026

Kodi mukudziwa kuti ife ndife akatswiri okonza mipando yakale kukhalanso yatsopano. Ngakahale kusintha deisgn zimatheka. Mitengo imatengera design yanu. Tatiyeseni simuzakhumudwa

Lilongwe

Phone πŸ“ž 0999629159

07/05/2026

Ma set a clean osamba. Mk400000 umodzi zatengeni. Mukambirane kulipo

Tiyankhuleni pa 0999629159

Photos from Starise Furniture & Home Decor's post 06/05/2026

Tikuthokoza onse amene amapanga share ma post athu. We don’t take it for granted. Christina Wa Mike Banda ndi Mphatso Muliya ndi Emmily Makina kwa week ino inu atatu mwapanga share ma post athu Kwambiri muzatenge flower pot imodzi imodzi ku shop kwathu πŸ₯°πŸ₯°

Photos from Starise Furniture & Home Decor's post 06/05/2026

Tangoyesani kupeza iti mukaike pa mpando pa living room panu mukaone kuwala kwake. Zosaboola mthumba izi.

Prices are for covers only

Fikani shop yathu ili mu area 4 Chimambula pafupi ndi Cashbuild orange building opposite Malawi housing shop #7

Phone 0999629159

Google Map: https://maps.google.com/?q=-13.974011,33.776131

Photos from Starise Furniture & Home Decor's post 05/05/2026

Zagule flower pot partner nyumba ikongole πŸ₯°πŸ₯° mitengo ili pa ma photos pomwepo.

Tipezeni ku Lilongwe area 4 Chilambula pafupi ndi Cashbuild power pali Sunset funeral services shop #7

0999629159

Want your business to be the top-listed Furniture Store in Lilongwe Area 18?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Babtist Church
Lilongwe Area 18