K Tech Electronic Store

K Tech Electronic Store

Share

Stockist of original reputable Bluetooth speakers, Smart phones, chargers, earpods and many more excellence, served with heart the best customer maker.

your satisfaction is our obligation! Whatsapp or call 0998045133

Photos from K Tech Electronic Store's post 04/06/2026

Paja ife timakonda kunena kuti palibe chifukwa choti Inu komanso achibale any akhalire opanda phone chifukwa ife timapezeka ndi ma phone a mitengo yonse komaso ma space onse

Tiimbireni pa 0998045133, tili Lilongwe area 3

19/05/2026

📱ORIGINAL SAMSUNG Z FOLD 5G
🟦256GB STORAGE
🟩12 GB RAM

🏷️MK 2,550,000

19/05/2026

📱 *ORIGINAL SAMSUNG GALAXY S23 FE 5G
*
🟦256GB Storage
🟩8GB Ram
📸50 mp main. Camera

_💰MK 1,400,000_

19/05/2026

ORIGINAL BRANDNEW VIVO X90 📱📸

The iconic vivo zeiss HD 📸 📸

🟦256 GB STORAGE
🟩12 GB RAM

💰MK 1,350,000

Lilongwe
0998045133

19/05/2026

🔥 BUSSINESS MACHINE, GAMING MACHINE 🎮
*⚙️ ONEPLUS ACE 2

SUBMITTING TO ALL THE HEAVY BUSSINESS PHONE USERS AND GAMERS

🟦512GB Storage
🟩12GB+12GB Ram

octa-core (8-core) processor. Qualcomm Snapdragon 8+ Gen 1 (4 nm) chipset🔥🥵

120Hz refresh rate

💰💵 MK 1,380,000

Lilongwe
,0998045133

19/05/2026

ORIGINAL GALAXY S23 ULTRA 📱

🟦256GB Storage
🟩12GB Ram

💰K 1,950,000

Lilongwe
Call or whatsapp 0998045133 to buy

19/05/2026

ORIGINAL GALAXY S24 ULTRA 📱

🟦256GB Storage
🟩12GB Ram

💰K 3,000,000

Lilongwe
0998045133

15/05/2026

AKASI mwaswera bwanji? Anthufe ndiosiyana mu zokonda, Pali anthu amene amafuna amangofunsa basi, chitseko choti chongotsekula ndi kutseka, chitseko choti anthu bola asamaone zili nkatimo.

Koma palinso anthu ena amene amafuna chitseko choti chizilankhula, inde kukamba za class, ulemerero ndi mmene moyo wawo ulili. Izi si zitseko zongoti bola chikutseka iyayi. Izi ndi zitseko za anthu amene akufuna nyumba yawo izioneka yolemekezeka ngakhale munthu asanalowe mkati.

Mukafika pa nyumba choyamba anthu mmaona ndi chitseko. Ndipo chitseko chanu chimauza anthu mtundu wa munthu amene amakhala m’nyumbamo.

Ngati mukufuna za chisawawa nde kuli zitseko zambiri kunjaku. Koma ngati mukufuna nyumba yomwe imatulutsa status ndi class ma doors awa ndi anu.

Ife a Yankho Furniture timakhulupilila kuti nyumba yabwino imayambira pa first impression. Tipezeni mudzagule chanu relo.

✔️ Strong hardwood
✔️ Premium finishing
✔️ Clean modern design
✔️ Door yomwe imapatsa nyumba presence

Want your business to be the top-listed Furniture Store in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Lilongwe