Zochitika ku Chiringa and Breaking News

Zochitika ku Chiringa and Breaking News

Share

Nkhani zongochitika kumene ndi zina zabwino zoti titha kugawana.

01/06/2026

Nkhani yachisoni:

Taluza mmbale wathu mu Chiringa muno Mr Mukoko,.

Mr Mukoko anasamukira ku Mozambique komwe amapanga ma business awo kumeneko.

Achita ngozi ya njinga yamito pa Phelani.

Nzimu wawo uwuse mu ntendere.

27/05/2026

KUMADZICHEPETSA PALIBE AMADZIWA MAWA!! ๐Ÿ™Œ๐Ÿ”ฅ

Meet Paul Lomoliwa, former member wa Community Policing Forum ku Phalombe.

Lero wachoka pa kukhala membala wa Community Policing Forum mpaka kukhala Police Constable ๐Ÿ‘ฎ๐Ÿพโ€โ™‚๏ธ๐Ÿ‘
Congratulations Paul Lomoliwa. Ulendo wako ukuonetsa kuti kuleza mtima, kudzichepetsa ndi kugwira ntchito mwakhama zimabala zipatso. Stay humble people ๐Ÿ™

๐Ÿ“– โ€˜Pakuti wodzichepetsa adzakwezedwa.โ€™ โ€” Luka 14:

18/05/2026

Team yanu ilipati? ๐Ÿคท

17/05/2026

ANTHU AKU PHALOMBE VUTO NDI CHANI?

Pholo ili ladulidwa nsewu wa MPATA ku Phalombe Boma, kuchita kuwonetselatu kuti anafasa ndithu kudula ndi SAW.

Izizi ndiza bwino?
Mesa zikuthandiza ife tomwe?
Umbuli wamtundu wanji uwu?

17/05/2026

Ife kwathu ndi kwa Petrol Mora nankha inu?

Send a message to learn more

17/05/2026

Yavuta ndi 200,000,000. Ma team apwetekana๐Ÿคท๐Ÿ˜…

17/05/2026


Anthu atatu m'boma la Phalombe apezeka ndi matenda a Kolera

Happy Chawinga mneneri mu ofesi ya zaumoyo m'bomali wasimikiza za nkhaniyi poyankhula ndi Phalombe fm.

Chawinga wati anthu atatuwa amachokera dera la Nkhulambe lomwe lachita malire ndi dziko la Mozambique.

Apa iye wapempha anthu kugwirana manja polimbana ndi nthendayi ndikuwonetsetsa kuti njira zonse zothandizira kupewa kufalikira Kwa matendawa zikutsatiridwa.

Copied.

16/05/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Harry Manyamba, Eliza Seleman, Lloyd Maganga, Victor Chimbax, Abdul Cassim, Lucy Hassan, Vidda Sankhulani, Prince Haleke, Lonney Chilumpha, Mangwinji Sondolo

15/05/2026

Ma galimoto wo basi tulutsani.

14/05/2026

Taluza mmodzi mwa ma Nurse athu mu Phalombe muno"Peter Mbelenga" pa ngozi. Nzimu wake uwuse mu ntendere ๐Ÿ˜ญ

Want your business to be the top-listed Furniture Store in Phalombe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Lolo Nazombe Phalombe
Phalombe